
Wanderers yaswa MAFCO pa Kamuzu, Songwe ikugawabe ma point
Timu ya Mighty wanderers yagonjetsa timu ya Malawi Armed Forces College MAFCO 2-0 pa bwalo la Kamuzu mu TNM Super League. Chigoli chomwe chikhonza kukhala cha mwamsanga kwambiri chiyambileni League pa mphindi yachitatu mpira utangoyamba, osewela wakale wa …